Oweruza 9:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Tsopano Abimeleki anapita ku Tebezi+ kumene anamenyana ndi mzindawo n’kuulanda.