-
Oweruza 9:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 Popeza pakati pa mzindawo panali nsanja yolimba, amuna ndi akazi onse, nzika zonse za mzindawo, zinathawira munsanjayo. Atalowa mmenemo, anatseka chitseko ndi kukwera padenga la nsanjayo.
-