-
Oweruza 12:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Yefita anaweruza Isiraeli zaka 6. Kenako Yefita wa ku Giliyadiyo anamwalira ndipo anaikidwa m’manda mumzinda wakwawo ku Giliyadi.
-