-
Oweruza 12:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ibizani anabereka ana aamuna 30 ndi ana aakazi 30. Iye anatuma anthu kukatenga atsikana 30 kuchokera kwina kuti akhale akazi a ana ake. Ndipo anaweruza Isiraeli kwa zaka 7.
-