Oweruza 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo pa Eloni, Abidoni mwana wa Hilele wa ku Piratoni,+ anayamba kuweruza Isiraeli.