-
Oweruza 17:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Pamenepo Mika anam’funsa kuti: “Wachokera kuti?” Poyankha, iye anati: “Ine ndine Mlevi. Ndachokera ku Betelehemu wa ku Yuda, ndipo ndikupita kulikonse kumene ndingapeze malo okhala, kuti ndikakhale kumeneko kwa kanthawi.”
-