Oweruza 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo anali kunena kuti: “N’chifukwa chiyani chinthu chimenechi chachitika mu Isiraeli, inu Yehova Mulungu wa Isiraeli? N’chifukwa chiyani lero fuko limodzi lasowa mu Isiraeli?”+
3 Iwo anali kunena kuti: “N’chifukwa chiyani chinthu chimenechi chachitika mu Isiraeli, inu Yehova Mulungu wa Isiraeli? N’chifukwa chiyani lero fuko limodzi lasowa mu Isiraeli?”+