-
Oweruza 21:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Abambo awo kapena abale awo akabwera kudzatiimba mlandu, tidzawauza kuti, ‘Tikomereni mtima powathandiza iwowa, chifukwa chakuti panthawi ya nkhondo, ife sitinagwire akazi okwanira Abenjamini onse.+ Ndipotu inu simunawapatse ana anuwo kapena alongo anuwo mwa kufuna kwanu, zimene zikanachititsa kuti mukhale ndi mlandu chifukwa cha lumbiro limene tinapanga lija.’”+
-