Oweruza 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero ana a Benjamini anachitadi zomwezo. Pakati pa akazi amene anali kuvina+ mozungulira, anagwirapo akazi okwanira chiwerengero chawo.+ Atatero, anachoka ndi kubwerera kumalo awo ndipo anamanga mizinda+ ndi kukhalamo.
23 Chotero ana a Benjamini anachitadi zomwezo. Pakati pa akazi amene anali kuvina+ mozungulira, anagwirapo akazi okwanira chiwerengero chawo.+ Atatero, anachoka ndi kubwerera kumalo awo ndipo anamanga mizinda+ ndi kukhalamo.