Rute 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Panali munthu wina wolemera kwambiri+ yemwe anali wachibale+ wa mwamuna wake wa Naomi. Dzina lake anali Boazi,+ wa kubanja la Elimeleki.
2 Panali munthu wina wolemera kwambiri+ yemwe anali wachibale+ wa mwamuna wake wa Naomi. Dzina lake anali Boazi,+ wa kubanja la Elimeleki.