Rute 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Boazi anauza Rute kuti: “Tamvera mwana wanga, usapitenso kumunda wina kukakunkha.+ Usachoke pano kupita kwina, ukhale pafupi ndi atsikana anga antchitowa.+ Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2016, tsa. 3
8 Kenako Boazi anauza Rute kuti: “Tamvera mwana wanga, usapitenso kumunda wina kukakunkha.+ Usachoke pano kupita kwina, ukhale pafupi ndi atsikana anga antchitowa.+