Rute 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atamva zimenezo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Zatheka bwanji kuti mundiganizire ndi kundikomera mtima chotere, ine wokhala mlendo?”+
10 Atamva zimenezo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Zatheka bwanji kuti mundiganizire ndi kundikomera mtima chotere, ine wokhala mlendo?”+