Rute 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo Naomi+ anauza Rute mpongozi wake+ kuti: “Ndi bwinodi mwana wanga, uzipita limodzi ndi atsikana akewo, kuopera kuti angakakunyoze ukapita kumunda wina.”+ Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:22 Tsanzirani, ptsa. 43-44 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, tsa. 20
22 Ndipo Naomi+ anauza Rute mpongozi wake+ kuti: “Ndi bwinodi mwana wanga, uzipita limodzi ndi atsikana akewo, kuopera kuti angakakunyoze ukapita kumunda wina.”+