Rute 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho Rute anapitiriza kukhala pafupi ndi atsikana antchito a Boazi, mpaka pamene anamaliza kukolola balere+ ndi tirigu. Ndipo anapitiriza kukhala ndi apongozi ake.+ Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:23 Tsanzirani, ptsa. 43-44 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, tsa. 20
23 Choncho Rute anapitiriza kukhala pafupi ndi atsikana antchito a Boazi, mpaka pamene anamaliza kukolola balere+ ndi tirigu. Ndipo anapitiriza kukhala ndi apongozi ake.+