1 Samueli 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno mutenge likasa la Yehova ndi kuliika m’ngoloyo. Zinthu zagolide+ zimene muyenera kupereka monga nsembe ya kupalamula+ muziike m’bokosi lina pambali pa likasa, kenako mulitumize, ndipo lichoke.
8 Ndiyeno mutenge likasa la Yehova ndi kuliika m’ngoloyo. Zinthu zagolide+ zimene muyenera kupereka monga nsembe ya kupalamula+ muziike m’bokosi lina pambali pa likasa, kenako mulitumize, ndipo lichoke.