1 Samueli 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Olamulira asanu ogwirizana+ a Afilisiti aja anaona zimenezo ndipo anabwerera ku Ekironi tsiku limenelo.
16 Olamulira asanu ogwirizana+ a Afilisiti aja anaona zimenezo ndipo anabwerera ku Ekironi tsiku limenelo.