1 Samueli 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamapeto pake anatumiza mithenga kwa anthu a ku Kiriyati-yearimu+ kuti: “Afilisiti abweza likasa la Yehova, bwerani kuno mudzalitenge.”+
21 Pamapeto pake anatumiza mithenga kwa anthu a ku Kiriyati-yearimu+ kuti: “Afilisiti abweza likasa la Yehova, bwerani kuno mudzalitenge.”+