1 Samueli 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mmodzi wa iwo poyankha anati: “Koma kodi bambo wawo ndani?” N’chifukwa chake pali mawu okuluwika+ akuti: “Kodi Sauli nayenso ndi mmodzi wa aneneri?”
12 Mmodzi wa iwo poyankha anati: “Koma kodi bambo wawo ndani?” N’chifukwa chake pali mawu okuluwika+ akuti: “Kodi Sauli nayenso ndi mmodzi wa aneneri?”