1 Samueli 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Poyankha Sauli anati: “Anthuwa+ azitenga kwa Aamaleki, chifukwa sanaphe nkhosa ndi ng’ombe zabwino kwambirizi n’cholinga chofuna kuzipereka nsembe kwa Yehova Mulungu wanu.+ Koma zina zonse zotsala taziwononga.”
15 Poyankha Sauli anati: “Anthuwa+ azitenga kwa Aamaleki, chifukwa sanaphe nkhosa ndi ng’ombe zabwino kwambirizi n’cholinga chofuna kuzipereka nsembe kwa Yehova Mulungu wanu.+ Koma zina zonse zotsala taziwononga.”