1 Samueli 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye n’chifukwa chiyani sunamvere mawu a Yehova, koma unathamangira zofunkha mosusuka+ ndi kuyamba kuchita zinthu zoipa pamaso pa Yehova?”+
19 Ndiye n’chifukwa chiyani sunamvere mawu a Yehova, koma unathamangira zofunkha mosusuka+ ndi kuyamba kuchita zinthu zoipa pamaso pa Yehova?”+