1 Samueli 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo Sauli anayankha Samueli kuti: “Ndachimwa,+ ndaphwanya lamulo la Yehova komanso sindinamvere mawu anu, chifukwa ndinaopa anthu+ ndipo ndamvera mawu awo.
24 Pamenepo Sauli anayankha Samueli kuti: “Ndachimwa,+ ndaphwanya lamulo la Yehova komanso sindinamvere mawu anu, chifukwa ndinaopa anthu+ ndipo ndamvera mawu awo.