1 Samueli 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Tsopano Samueli ananyamuka kupita ku Rama, koma Sauli anapita kunyumba kwake ku Gibeya.+