1 Samueli 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Akisi anakhulupirira+ Davide, ndipo mumtima mwake anati: “Mosakayikira, Davide wakhala fungo lonunkha kwa anthu akwawo Aisiraeli,+ ndipo iye akhala mtumiki wanga mpaka kalekale.”
12 Akisi anakhulupirira+ Davide, ndipo mumtima mwake anati: “Mosakayikira, Davide wakhala fungo lonunkha kwa anthu akwawo Aisiraeli,+ ndipo iye akhala mtumiki wanga mpaka kalekale.”