1 Samueli 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Davide anati: “Ayi abale anga, musatero ndi zinthu zimene Yehova watipatsa.+ Iye watiteteza+ ndi kupereka m’manja mwathu gulu la achifwamba limene linadzatiukira.+
23 Koma Davide anati: “Ayi abale anga, musatero ndi zinthu zimene Yehova watipatsa.+ Iye watiteteza+ ndi kupereka m’manja mwathu gulu la achifwamba limene linadzatiukira.+