2 Samueli 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Rekabu ndi Bana, ana aamuna a Rimoni Mbeeroti, ananyamuka kupita kunyumba ya Isi-boseti+ masana kutatentha, ndipo anamupeza akugona.
5 Rekabu ndi Bana, ana aamuna a Rimoni Mbeeroti, ananyamuka kupita kunyumba ya Isi-boseti+ masana kutatentha, ndipo anamupeza akugona.