2 Samueli 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo analowa m’nyumbamo ngati anthu ofuna tirigu, kenako anakantha Isi-boseti pamimba.+ Atatero, Rekabu ndi m’bale wake Bana+ anathawa kuti asadziwike.
6 Iwo analowa m’nyumbamo ngati anthu ofuna tirigu, kenako anakantha Isi-boseti pamimba.+ Atatero, Rekabu ndi m’bale wake Bana+ anathawa kuti asadziwike.