2 Samueli 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo atalowa m’nyumbamo, anapeza Isi-boseti atagona pabedi m’chipinda chake, ndipo anamukantha ndi kumupha.+ Kenako anamudula mutu+ ndipo anautenga ndi kuyenda nawo usiku wonse mumsewu wopita ku Araba.
7 Iwo atalowa m’nyumbamo, anapeza Isi-boseti atagona pabedi m’chipinda chake, ndipo anamukantha ndi kumupha.+ Kenako anamudula mutu+ ndipo anautenga ndi kuyenda nawo usiku wonse mumsewu wopita ku Araba.