3 Koma akalonga a ana a Amoni anauza Hanuni mbuye wawo kuti: “Kodi ukuganiza kuti Davide watumiza anthu odzakutonthoza kuti alemekeze bambo ako pamaso pako? Kodi iye sanatumize atumiki akewa kwa iwe kuti adzaonetsetse mzindawu ndi kuchita ukazitape,+ kuti adzaulande?”+