-
2 Samueli 10:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Pambuyo pake anthu anauza Davide zimene zinachitika, ndipo iye nthawi yomweyo anatumiza anthu kuti akakumane ndi atumiki akewo chifukwa atumikiwo anaona kuti awachititsa manyazi kwambiri. Choncho mfumu inawauza kuti: “Mukhalebe ku Yeriko+ kufikira ndevu zanu zitachuluka ndithu, kenako mudzabwere.”
-