-
2 Samueli 11:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Uriya atafika kwa Davide, Davideyo anayamba kumufunsa za umoyo wa Yowabu, za umoyo wa anthu ndi mmene nkhondo inali kuyendera.
-