2 Samueli 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako Ahimazi anaitana mfumu ndi kuiuza kuti: “Zonse zili bwino!” Atatero anagwada pamaso pa mfumu ndi kuwerama. Ndiyeno anati: “Adalitsike+ Yehova Mulungu wanu, amene wapereka+ amuna amene anatambasula manja awo ndi kuukira inu mbuyanga mfumu!”
28 Kenako Ahimazi anaitana mfumu ndi kuiuza kuti: “Zonse zili bwino!” Atatero anagwada pamaso pa mfumu ndi kuwerama. Ndiyeno anati: “Adalitsike+ Yehova Mulungu wanu, amene wapereka+ amuna amene anatambasula manja awo ndi kuukira inu mbuyanga mfumu!”