1 Mafumu 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mfumu Solomo ndi msonkhano wonse wa Isiraeli, onse amene anabwera atawaitana, anafika pamaso pa Likasa n’kuyamba kupereka nsembe+ zambiri za nkhosa ndi ng’ombe, zomwe sanathe kuziwerenga chifukwa chochuluka.+
5 Mfumu Solomo ndi msonkhano wonse wa Isiraeli, onse amene anabwera atawaitana, anafika pamaso pa Likasa n’kuyamba kupereka nsembe+ zambiri za nkhosa ndi ng’ombe, zomwe sanathe kuziwerenga chifukwa chochuluka.+