1 Mafumu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba,+ simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba+ imene ndamangayi? 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:27 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
27 “Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba,+ simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba+ imene ndamangayi?