1 Mafumu 8:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Muchite zimenezi n’cholinga choti iwo akuopeni,+ masiku onse amene angakhale ndi moyo padziko limene munapatsa makolo athu.+
40 Muchite zimenezi n’cholinga choti iwo akuopeni,+ masiku onse amene angakhale ndi moyo padziko limene munapatsa makolo athu.+