2 Mafumu 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo atalandira makalatawo anachita mantha kwambiri, ndipo anayamba kunena kuti: “Mafumu+ awiri sanathe kulimbana naye, nanga ifeyo tingalimbane naye bwanji?”+
4 Iwo atalandira makalatawo anachita mantha kwambiri, ndipo anayamba kunena kuti: “Mafumu+ awiri sanathe kulimbana naye, nanga ifeyo tingalimbane naye bwanji?”+