2 Mafumu 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno kunabwera mthenga+ kudzauza Yehu kuti: “Mitu ya ana+ a mfumu ija abwera nayo.” Pamenepo Yehu anati: “Kaiunjikeni milu iwiri pachipata, ndipo ikhale pamenepo kufikira m’mawa.”+
8 Ndiyeno kunabwera mthenga+ kudzauza Yehu kuti: “Mitu ya ana+ a mfumu ija abwera nayo.” Pamenepo Yehu anati: “Kaiunjikeni milu iwiri pachipata, ndipo ikhale pamenepo kufikira m’mawa.”+