2 Mafumu 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Yehu ndi Yehonadabu+ mwana wa Rekabu analowa m’kachisi wa Baala. Tsopano Yehu anauza olambira a Baala kuti: “Fufuzani mosamala, ndipo muonetsetse kuti muno musakhale wolambira wa Yehova aliyense, koma olambira a Baala okha.”+
23 Kenako Yehu ndi Yehonadabu+ mwana wa Rekabu analowa m’kachisi wa Baala. Tsopano Yehu anauza olambira a Baala kuti: “Fufuzani mosamala, ndipo muonetsetse kuti muno musakhale wolambira wa Yehova aliyense, koma olambira a Baala okha.”+