2 Mafumu 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova monga anachitira makolo ake.+ Sanasiye machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+
9 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova monga anachitira makolo ake.+ Sanasiye machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+