1 Mbiri 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Kalebe+ mwana wa Yefune+ anali Iru, Ela, ndi Naamu. Mwana wa Ela anali Kenazi.