1 Mbiri 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Simeyi anali ndi ana aamuna 16 ndi ana aakazi 6, koma abale ake analibe ana ambiri. Palibe banja lawo lililonse limene linali ndi ana ambiri ngati mabanja a ana a Yuda.+
27 Simeyi anali ndi ana aamuna 16 ndi ana aakazi 6, koma abale ake analibe ana ambiri. Palibe banja lawo lililonse limene linali ndi ana ambiri ngati mabanja a ana a Yuda.+