1 Mbiri 12:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anthuwa anakhala kumeneko ndi Davide masiku atatu. Anali kudya ndi kumwa,+ chifukwa abale awo anali atawakonzekera.
39 Anthuwa anakhala kumeneko ndi Davide masiku atatu. Anali kudya ndi kumwa,+ chifukwa abale awo anali atawakonzekera.