1 Mbiri 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako tikatenge likasa+ la Mulungu wathu n’kubwera nalo mpaka kwathu kuno.” Anatero chifukwa chakuti m’masiku a Sauli likasalo sanali kulisamala.+
3 Kenako tikatenge likasa+ la Mulungu wathu n’kubwera nalo mpaka kwathu kuno.” Anatero chifukwa chakuti m’masiku a Sauli likasalo sanali kulisamala.+