10 Yowabu ataona kuti asilikali a adani ake akubwera mofulumira kuchokera kutsogolo ndi kumbuyo kudzamenyana naye, nthawi yomweyo anatenga amuna ochita kusankhidwa mwapadera a mu Isiraeli ndipo anafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo kuti akumane ndi Asiriya.+