1 Mbiri 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uchite zinthu mwamphamvu,+ ndipo tisonyeze kulimba mtima chifukwa cha anthu athu, ndiponso chifukwa cha mizinda ya Mulungu wathu.+ Yehova adzachita zimene zili zabwino m’maso mwake.”+
13 Uchite zinthu mwamphamvu,+ ndipo tisonyeze kulimba mtima chifukwa cha anthu athu, ndiponso chifukwa cha mizinda ya Mulungu wathu.+ Yehova adzachita zimene zili zabwino m’maso mwake.”+