1 Mbiri 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Asiriya ataona kuti agonjetsedwa+ ndi Aisiraeli, anatumiza amithenga kukaitana Asiriya amene anali m’dera la ku Mtsinje,*+ pamodzi ndi Sofaki mtsogoleri wa gulu lankhondo la Hadadezeri.
16 Asiriya ataona kuti agonjetsedwa+ ndi Aisiraeli, anatumiza amithenga kukaitana Asiriya amene anali m’dera la ku Mtsinje,*+ pamodzi ndi Sofaki mtsogoleri wa gulu lankhondo la Hadadezeri.