1 Mbiri 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Benaya+ ameneyu anali mwamuna wamphamvu pa amuna 30+ komanso anali mtsogoleri wa amuna 30 amenewo. Pagulu lakelo, mwana wake Amizabadi ndiye anali mtsogoleri.
6 Benaya+ ameneyu anali mwamuna wamphamvu pa amuna 30+ komanso anali mtsogoleri wa amuna 30 amenewo. Pagulu lakelo, mwana wake Amizabadi ndiye anali mtsogoleri.