1 Mbiri 27:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kuwonjezera pa Ahitofeli panalinso Yehoyada mwana wa Benaya+ ndi Abiyatara,+ ndipo Yowabu+ anali mkulu wa asilikali a mfumu.
34 Kuwonjezera pa Ahitofeli panalinso Yehoyada mwana wa Benaya+ ndi Abiyatara,+ ndipo Yowabu+ anali mkulu wa asilikali a mfumu.