1 Mbiri 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa chakuti ndikusangalala+ ndi nyumba ya Mulungu wanga, ndili ndi chuma chapadera+ chomwe ndi golide ndi siliva. Ndikupereka chuma chimenechi kunyumba ya Mulungu wanga kuwonjezera pa zonse zimene ndakonzera nyumba yopatulikayo.+
3 Chifukwa chakuti ndikusangalala+ ndi nyumba ya Mulungu wanga, ndili ndi chuma chapadera+ chomwe ndi golide ndi siliva. Ndikupereka chuma chimenechi kunyumba ya Mulungu wanga kuwonjezera pa zonse zimene ndakonzera nyumba yopatulikayo.+