1 Mbiri 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inu Yehova Mulungu wathu, zinthu zochuluka zonsezi zimene takonzekera kuti tikumangireni nyumba, nyumba ya dzina lanu loyera, zachokera m’dzanja lanu ndipo zonse ndi zanu.+
16 Inu Yehova Mulungu wathu, zinthu zochuluka zonsezi zimene takonzekera kuti tikumangireni nyumba, nyumba ya dzina lanu loyera, zachokera m’dzanja lanu ndipo zonse ndi zanu.+