1 Mbiri 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mupatse Solomo mwana wanga mtima wathunthu+ kuti asunge malamulo anu,+ maumboni* anu,+ ndi kuti achite zonse. Ndiponso kuti amange chinyumba chachikulu+ chimene ndakonzeratu zipangizo zake.”+
19 Mupatse Solomo mwana wanga mtima wathunthu+ kuti asunge malamulo anu,+ maumboni* anu,+ ndi kuti achite zonse. Ndiponso kuti amange chinyumba chachikulu+ chimene ndakonzeratu zipangizo zake.”+